Yobu 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mawu a atsogoleri ankabisika,Ndipo lilime lawo linkamamatira m’kamwa mwawo.+