Yobu 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muzu wanga ndi wotseguka kuti uyamwe madzi,+Ndipo mame akhala usiku wonse panthambi yanga.