Yobu 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu amabangula ndi mawu ake+ mochititsa chidwi kwambiri.Amachita zinthu zazikulu zimene sitingazidziwe.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:5 Nsanja ya Olonda,4/15/2001, tsa. 4
5 Mulungu amabangula ndi mawu ake+ mochititsa chidwi kwambiri.Amachita zinthu zazikulu zimene sitingazidziwe.+