Salimo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+
11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+