Salimo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndidzaitanira pa Yehova, Iye woyenera kutamandidwa,+Ndipo adzandipulumutsa kwa adani anga.+