Salimo 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti inu Yehova mudzandiyatsira nyale yanga,+Mulungu wanga adzandiunikira mu mdima.+