Salimo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndine nyongolotsi+ osati munthu.Anthu amanditonza ndipo ndine wonyozeka kwa anthu.+