Salimo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndingathe kuwerenga mafupa anga onse.+Adaniwo akuona zimenezi, ndipo akundiyang’anitsitsa.+