Salimo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+
7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+