Salimo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2017, ptsa. 8-12 Nsanja ya Olonda,3/1/2007, tsa. 29
22 Yehova amawombola moyo wa atumiki ake.+Ndipo palibe aliyense wothawira kwa iye amene adzapezeka wolakwa.+