1 Mafumu 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mfumuyo inalumbira+ kuti: “Pali Yehova+ amene anapulumutsa+ moyo wanga+ m’masautso onse,+ Salimo 71:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani. Salimo 103:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+ Maliro 3:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Inu Yehova, mwandiweruzira milandu yanga.+ Mwawombola moyo wanga.+
23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani.
4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+ Maliro 3:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Inu Yehova, mwandiweruzira milandu yanga.+ Mwawombola moyo wanga.+