Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ochita zoipa adzaphedwa.+Koma oyembekezera Yehova ndi amene adzalandire dziko lapansi.+