Salimo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti manja a anthu oipa adzathyoledwa,+Koma Yehova adzathandiza anthu olungama.+