Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:1 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 10
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+