Salimo 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti zolakwa zanga ndikuzidziwa bwino,+Ndipo tchimo langa lili pamaso panga nthawi zonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:3 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 11