Salimo 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeretseni ndi hisope ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa chipale chofewa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:7 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 12
7 Ndiyeretseni ndi hisope ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa chipale chofewa.+