Salimo 56:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+
12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+