Salimo 59:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+
3 Pakuti, taonani! Iwo akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+Inu Yehova, anthu amphamvu akundiukira,+Ngakhale kuti ine sindinapanduke kapena kuchita tchimo lililonse.+