Salimo 59:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mphamvu yanga, ine ndidzaimba nyimbo zokutamandani,+Pakuti Mulungu ndiye malo anga okwezeka ndiponso achitetezo, Mulungu wandisonyeza kukoma mtima kosatha.+
17 Inu Mphamvu yanga, ine ndidzaimba nyimbo zokutamandani,+Pakuti Mulungu ndiye malo anga okwezeka ndiponso achitetezo, Mulungu wandisonyeza kukoma mtima kosatha.+