Salimo 65:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mizere yawo imakhathamira, ndipo zibuma zake zimasalazidwa,+Ndipo mumafewetsa nthaka ndi mvula yamvumbi. Mumadalitsa zomera m’nthakayo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:10 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 175
10 Mizere yawo imakhathamira, ndipo zibuma zake zimasalazidwa,+Ndipo mumafewetsa nthaka ndi mvula yamvumbi. Mumadalitsa zomera m’nthakayo.+