Salimo 69:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ine ndasautsika ndipo ndikumva kupweteka.+Inu Mulungu, chipulumutso chanu chinditeteze.+