Salimo 72:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+
72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+