Salimo 72:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo.
3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo.