Salimo 72:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+
15 Iye akhale ndi moyo wautali,+ ndipo apatsidwe wina mwa golide wa ku Sheba.+Nthawi zonse anthu azimupempherera.Adalitsike tsiku lililonse.+