Salimo 74:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu amene akukuchitirani zoipa afuula mosangalala kuti apambana m’malo anu olambiriramo.+Aikamo mbendera zawo monga zizindikiro.+
4 Anthu amene akukuchitirani zoipa afuula mosangalala kuti apambana m’malo anu olambiriramo.+Aikamo mbendera zawo monga zizindikiro.+