Salimo 74:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbukirani pangano limene munachita nafe,+Pakuti malo a mdima a dziko lapansi adzaza ndi chiwawa.+
20 Kumbukirani pangano limene munachita nafe,+Pakuti malo a mdima a dziko lapansi adzaza ndi chiwawa.+