Salimo 78:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 78 Inu anthu anga, mvetserani chilamulo changa.+Tcherani khutu ku mawu a pakamwa panga.+