Salimo 78:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti anawo azidzadalira Mulungu,+Ndi kuti asadzaiwale zochita za Mulungu+ koma kuti azidzasunga malamulo ake.+
7 Kuti anawo azidzadalira Mulungu,+Ndi kuti asadzaiwale zochita za Mulungu+ koma kuti azidzasunga malamulo ake.+