Salimo 78:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+
19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+