Salimo 78:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anadya ndi kukhuta kwambiri.+Iye anawabweretsera zimene anali kulakalaka.+