Salimo 78:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma iwo anali kufuna kum’pusitsa ndi pakamwa pawo.+Ndi lilime lawo anali kufuna kunena bodza kwa iye.+
36 Koma iwo anali kufuna kum’pusitsa ndi pakamwa pawo.+Ndi lilime lawo anali kufuna kunena bodza kwa iye.+