Salimo 78:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anapereka zokolola zawo kwa mphemvu,Ndipo ntchito yawo yolemetsa anaipereka kwa dzombe.+