Salimo 78:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo Yehova anagalamuka ngati akudzuka kutulo,+Ngati munthu wamphamvu amene akugalamuka pambuyo pomwa vinyo wambiri.+
65 Pamenepo Yehova anagalamuka ngati akudzuka kutulo,+Ngati munthu wamphamvu amene akugalamuka pambuyo pomwa vinyo wambiri.+