Salimo 78:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Iye anathamangitsa adani ake ndi kuwapha.+Anawachititsa kuti akhale akutonzedwa mpaka kalekale.+