Salimo 83:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 83:1 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, tsa. 13
83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+