Salimo 83:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti ndi mtima wonse, iwo amagawana nzeru,+Ndipo anapangana pangano lotsutsana ndi inu.+