Salimo 86:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, tsa. 13
9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+