Salimo 86:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:14 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, tsa. 17
14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+