Salimo 92:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu oipa akamaphuka ngati msipu,+Ndipo anthu onse ochita zopweteka anzawo akamaphuka ngati maluwa,Amatero kuti awonongeke kwamuyaya.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 92:7 Galamukani!,No. 1 2021 tsa. 12
7 Anthu oipa akamaphuka ngati msipu,+Ndipo anthu onse ochita zopweteka anzawo akamaphuka ngati maluwa,Amatero kuti awonongeke kwamuyaya.+