Salimo 94:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti zigamulo zidzayambiranso kukhala zachilungamo,+Ndipo onse owongoka mtima adzazitsatira.