Salimo 119:142 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 142 Chilungamo chanu ndi chilungamo mpaka kalekale,+Ndipo chilamulo chanu ndi choonadi.+