Salimo 126:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+
2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+