Yesaya 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo adzasonkhanitsidwa ngati akaidi amene akuwasonkhanitsira m’dzenje.+ Adzatsekeredwa m’ndende,+ ndipo pakadzapita masiku ochuluka adzakumbukiridwanso.+ Yesaya 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+ Yeremiya 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero anatulutsa Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. Ndipo Yeremiya anapitiriza kukhala m’Bwalo la Alonda.+
22 Iwo adzasonkhanitsidwa ngati akaidi amene akuwasonkhanitsira m’dzenje.+ Adzatsekeredwa m’ndende,+ ndipo pakadzapita masiku ochuluka adzakumbukiridwanso.+
7 kuti ukatsegule maso a akhungu,+ ukatulutse mkaidi m’ndende ya mdima+ ndiponso kuti ukatulutse m’ndende anthu amene ali mu mdima.+
13 Zitatero anatulutsa Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. Ndipo Yeremiya anapitiriza kukhala m’Bwalo la Alonda.+