Salimo 146:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+
8 Yehova amatsegula maso a anthu akhungu.+Yehova amaweramutsa anthu owerama chifukwa cha masautso.+Yehova amakonda anthu olungama.+