Salimo 146:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+
9 Yehova amayang’anira alendo okhala m’dziko la eni.+Amathandiza mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.+Koma njira+ ya anthu oipa amaichititsa kukhala yovuta kuyendamo.+