Salimo 149:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Isiraeli asangalale ndi Womupanga Wamkulu,+Ana a Ziyoni akondwere ndi Mfumu yawo.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 149:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,1/1/1986, tsa. 30