Miyambo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:6 Nsanja ya Olonda,4/15/1987, tsa. 24 Galamukani!,4/8/1988, tsa. 20
6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+