Miyambo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mdani wako akagwa usamasangalale ndipo akapunthwa, mtima wako usamakondwere,+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 195