Mlaliki 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso ndinali kuchitabe zinthu mwanzeru.+
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso ndinali kuchitabe zinthu mwanzeru.+