Mlaliki 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Masiku ake onse, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Komanso usiku mtima wake sugona.+ Izinso n’zachabechabe.
23 Masiku ake onse, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Komanso usiku mtima wake sugona.+ Izinso n’zachabechabe.